Numeri 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Nyamuka, Balaki iwe, tamvera. Ndimvetsere, iwe mwana wa Zipori. Numeri 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako analankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna amene maso ake atseguka,
18 Kenako Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Nyamuka, Balaki iwe, tamvera. Ndimvetsere, iwe mwana wa Zipori.
3 Kenako analankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna amene maso ake atseguka,