-
Numeri 22:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Koma mngelo wa Yehovayo anauza Balamu kuti: “Pita nawo limodzi anthuwa, koma ukanene zokhazo zimene ndikuuze.” Choncho Balamu anapitiriza ulendo wake limodzi ndi akalonga a Balakiwo.
-