-
Genesis 12:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Yehova anauza Abulamu kuti: “Samuka mʼdziko lako ndi kuchoka pakati pa abale ako ndipo usiye nyumba ya bambo ako. Upite kudziko limene ndidzakuonetse.+ 2 Ndidzakupangitsa kuti ukhale mtundu waukulu. Ndidzakudalitsa ndipo ndidzapangitsa kuti dzina lako litchuke. Komanso anthu ena adzadalitsidwa chifukwa cha iwe.+
-
-
Genesis 22:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno mngelo wa Yehova anaitana Abulahamu kachiwiri kuchokera kumwamba,
-