Numeri 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Balamu anayankha atumiki a Balakiwo kuti: “Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chilichonse chosemphana ndi zimene Yehova Mulungu wanga angandilamule, kaya chachingʼono kapena chachikulu.+
18 Koma Balamu anayankha atumiki a Balakiwo kuti: “Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chilichonse chosemphana ndi zimene Yehova Mulungu wanga angandilamule, kaya chachingʼono kapena chachikulu.+