Genesis 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova anauza Abulamu kuti: “Samuka mʼdziko lako ndi kuchoka pakati pa abale ako ndipo usiye nyumba ya bambo ako. Upite kudziko limene ndidzakuonetse.+ Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo wotemberera iwe ndidzamutemberera.+ Mabanja onse apadziko lapansi adzadalitsidwa* kudzera mwa iwe.”+
12 Yehova anauza Abulamu kuti: “Samuka mʼdziko lako ndi kuchoka pakati pa abale ako ndipo usiye nyumba ya bambo ako. Upite kudziko limene ndidzakuonetse.+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo wotemberera iwe ndidzamutemberera.+ Mabanja onse apadziko lapansi adzadalitsidwa* kudzera mwa iwe.”+