1 Mbiri 4:42, 43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Anthu ena a fuko la Simiyoni, amuna okwana 500, anapita kuphiri la Seiri+ ndipo amene ankawatsogolera anali Pelatiya, Neariya, Refaya ndi Uziyeli, ana a Isi. 43 Iwo anapha Aamaleki+ otsala omwe anathawa ndipo akukhala kumeneko mpaka lero. Ezekieli 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Ine ndidzabwezera Edomu pogwiritsa ntchito anthu anga Aisiraeli.+ Aisiraeliwo adzachitira Edomu mogwirizana ndi mkwiyo komanso ukali wanga, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndikuwabwezera,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’
42 Anthu ena a fuko la Simiyoni, amuna okwana 500, anapita kuphiri la Seiri+ ndipo amene ankawatsogolera anali Pelatiya, Neariya, Refaya ndi Uziyeli, ana a Isi. 43 Iwo anapha Aamaleki+ otsala omwe anathawa ndipo akukhala kumeneko mpaka lero.
14 ‘Ine ndidzabwezera Edomu pogwiritsa ntchito anthu anga Aisiraeli.+ Aisiraeliwo adzachitira Edomu mogwirizana ndi mkwiyo komanso ukali wanga, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndikuwabwezera,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’