Genesis 41:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Mwana woyambayo, Yosefe anamupatsa dzina lakuti Manase*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse ndi nyumba yonse ya bambo anga.”
51 Mwana woyambayo, Yosefe anamupatsa dzina lakuti Manase*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse ndi nyumba yonse ya bambo anga.”