Deuteronomo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukakweza maso anu kuthambo nʼkuona dzuwa, mwezi ndi nyenyezi, gulu lonse la zinthu zakuthambo, musakopeke nazo nʼkuyamba kuzigwadira komanso kuzitumikira.+ Yehova Mulungu wanu wazipereka kwa anthu onse okhala pansi pa thambo lonse.
19 Mukakweza maso anu kuthambo nʼkuona dzuwa, mwezi ndi nyenyezi, gulu lonse la zinthu zakuthambo, musakopeke nazo nʼkuyamba kuzigwadira komanso kuzitumikira.+ Yehova Mulungu wanu wazipereka kwa anthu onse okhala pansi pa thambo lonse.