Deuteronomo 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho mudziwe lero kuti Yehova Mulungu wanu awoloka patsogolo panu.+ Iye ndi moto wowononga+ ndipo adzawawononga. Adzawagonjetsa inu mukuona kuti mudzawathamangitse* mwamsanga ndi kuwawononga, mogwirizana ndi zimene Yehova anakulonjezani.+
3 Choncho mudziwe lero kuti Yehova Mulungu wanu awoloka patsogolo panu.+ Iye ndi moto wowononga+ ndipo adzawawononga. Adzawagonjetsa inu mukuona kuti mudzawathamangitse* mwamsanga ndi kuwawononga, mogwirizana ndi zimene Yehova anakulonjezani.+