Ekisodo 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa mngelo wanga adzakutsogolerani nʼkukulowetsani mʼdziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi ndipo ine ndidzawawononga.+
23 Chifukwa mngelo wanga adzakutsogolerani nʼkukulowetsani mʼdziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi ndipo ine ndidzawawononga.+