1 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola, ulemerero ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi zapadziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu ndi wanu, inu Yehova.+ Ndinu Wokwezeka ndiponso ndinu mutu pa onse. Salimo 145:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wamkulu komanso woyenera kutamandidwa kwambiri,+Palibe amene angamvetse ukulu wake.+
11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola, ulemerero ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi zapadziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu ndi wanu, inu Yehova.+ Ndinu Wokwezeka ndiponso ndinu mutu pa onse.