Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti sukufuna kusintha, ndipo ukusonyeza mtima wosalapa, Mulungu adzakulanga ndithu pa tsiku la mkwiyo wake akamadzaulula chiweruzo chake cholungama.+
5 Koma chifukwa chakuti sukufuna kusintha, ndipo ukusonyeza mtima wosalapa, Mulungu adzakulanga ndithu pa tsiku la mkwiyo wake akamadzaulula chiweruzo chake cholungama.+