Yesaya 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti: “Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga,Ndipo ndidzabwezera adani anga.+ Yesaya 59:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye adzawapatsa mphoto chifukwa cha zimene achita:+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango.+ Ndipo zilumba adzazipatsa chilango chogwirizana ndi zochita zawo.
24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti: “Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga,Ndipo ndidzabwezera adani anga.+
18 Iye adzawapatsa mphoto chifukwa cha zimene achita:+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango.+ Ndipo zilumba adzazipatsa chilango chogwirizana ndi zochita zawo.