Ekisodo 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Mose anauza Yehova kuti: “Anthuwa sangafike paphiri la Sinai, chifukwa inu munawachenjeza kale pamene munandiuza kuti: ‘Udule malire kuzungulira phiri ndipo muziliona kuti ndi lopatulika.’”+
23 Kenako Mose anauza Yehova kuti: “Anthuwa sangafike paphiri la Sinai, chifukwa inu munawachenjeza kale pamene munandiuza kuti: ‘Udule malire kuzungulira phiri ndipo muziliona kuti ndi lopatulika.’”+