Genesis 49:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Rubeni,+ iwe ndi mwana wanga woyamba kubadwa,+ nyonga yanga ndi poyambira mphamvu zanga zobereka. Unayenera kukhala ndi ulemu waukulu ndi mphamvu zochuluka.
3 Rubeni,+ iwe ndi mwana wanga woyamba kubadwa,+ nyonga yanga ndi poyambira mphamvu zanga zobereka. Unayenera kukhala ndi ulemu waukulu ndi mphamvu zochuluka.