7 Komanso iye anaika mʼnyumbayo chifaniziro cha mzati wopatulika+ chimene anapanga. Koma ponena za nyumbayo, Yehova anauza Davide ndi mwana wake Solomo kuti: “Mʼnyumba iyi ndiponso mu Yerusalemu, mzinda umene ndausankha pa mafuko onse a Isiraeli, ndidzaikamo dzina langa mpaka kalekale.+