Ekisodo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku lachitatu mʼmawa, kunachita mabingu ndi mphezi ndipo mtambo wakuda+ unakuta phiri. Kunamvekanso kulira kwamphamvu kwambiri kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, moti anthu onse mumsasawo anayamba kunjenjemera.+
16 Pa tsiku lachitatu mʼmawa, kunachita mabingu ndi mphezi ndipo mtambo wakuda+ unakuta phiri. Kunamvekanso kulira kwamphamvu kwambiri kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, moti anthu onse mumsasawo anayamba kunjenjemera.+