Ekisodo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Usatemberere* Mulungu+ kapena mtsogoleri* amene ali pakati pa anthu a mtundu wako.+ Levitiko 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musamalumbire zabodza mʼdzina langa+ nʼkuipitsa dzina la Mulungu wanu. Ine ndine Yehova.