Deuteronomo 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi pali anthu enanso amene anamvapo mawu a Mulungu akumveka kuchokera pamoto ngati mmene inuyo munawamvera nʼkukhalabe ndi moyo?+ Deuteronomo 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anakuchititsani kuti mumve mawu ake kuchokera kumwamba nʼcholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuti muone moto waukulu, ndipo munamva mawu ake kuchokera pamotowo.+
33 Kodi pali anthu enanso amene anamvapo mawu a Mulungu akumveka kuchokera pamoto ngati mmene inuyo munawamvera nʼkukhalabe ndi moyo?+
36 Anakuchititsani kuti mumve mawu ake kuchokera kumwamba nʼcholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuti muone moto waukulu, ndipo munamva mawu ake kuchokera pamotowo.+