Deuteronomo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ Yesaya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli.Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyenseNdipo sindifuna kuti aliyense azitamanda zifaniziro zogoba mʼmalo mwa ine.+ Zekariya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala Mfumu ya dziko lonse lapansi.+ Pa tsiku limenelo, Yehova adzakhala mmodzi+ ndipo dzina lake lidzakhala limodzi.+ Maliko 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu anayankha kuti: “Loyamba ndi lakuti, ‘Tamverani Aisiraeli inu, Yehova* Mulungu wathu ndi Yehova* mmodzi. Maliko 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mlembiyo ananena kuti: “Mphunzitsi, mwanena bwino mogwirizana ndi choonadi, ‘Iye ndi Mmodzi ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo iyeyo.’+ 1 Akorinto 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kwa ife Mulungu alipo mmodzi yekha,+ amene ndi Atate.+ Zinthu zonse zinachokera kwa iye, ndipo ifeyo ndife ake.+ Palinso Ambuye mmodzi, Yesu Khristu, amene zinthu zonse zinakhalapo kudzera mwa iye,+ ndipo ifeyo kudzera mwa iyeyo.
8 Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli.Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyenseNdipo sindifuna kuti aliyense azitamanda zifaniziro zogoba mʼmalo mwa ine.+
9 Yehova adzakhala Mfumu ya dziko lonse lapansi.+ Pa tsiku limenelo, Yehova adzakhala mmodzi+ ndipo dzina lake lidzakhala limodzi.+
29 Yesu anayankha kuti: “Loyamba ndi lakuti, ‘Tamverani Aisiraeli inu, Yehova* Mulungu wathu ndi Yehova* mmodzi.
32 Mlembiyo ananena kuti: “Mphunzitsi, mwanena bwino mogwirizana ndi choonadi, ‘Iye ndi Mmodzi ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo iyeyo.’+
6 Koma kwa ife Mulungu alipo mmodzi yekha,+ amene ndi Atate.+ Zinthu zonse zinachokera kwa iye, ndipo ifeyo ndife ake.+ Palinso Ambuye mmodzi, Yesu Khristu, amene zinthu zonse zinakhalapo kudzera mwa iye,+ ndipo ifeyo kudzera mwa iyeyo.