Maliko 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Muzikonda Yehova* Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, moyo wanu wonse, maganizo anu onse ndi mphamvu zanu zonse.’+ Maliko 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndipo kukonda Mulungu ndi mtima wonse, maganizo onse, mphamvu zonse komanso kukonda mnzako mmene umadzikondera wekha, nʼzofunika kwambiri kuposa nsembe zonse zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.”+ Luka 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anayankha kuti: “‘Muzikonda Yehova* Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, moyo wanu wonse, mphamvu zanu zonse ndi maganizo anu onse.’+ Komanso ‘uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’”+
30 Muzikonda Yehova* Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, moyo wanu wonse, maganizo anu onse ndi mphamvu zanu zonse.’+
33 Ndipo kukonda Mulungu ndi mtima wonse, maganizo onse, mphamvu zonse komanso kukonda mnzako mmene umadzikondera wekha, nʼzofunika kwambiri kuposa nsembe zonse zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.”+
27 Iye anayankha kuti: “‘Muzikonda Yehova* Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, moyo wanu wonse, mphamvu zanu zonse ndi maganizo anu onse.’+ Komanso ‘uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.’”+