-
Deuteronomo 6:14, 15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Musatsatire milungu ina, milungu iliyonse ya anthu amene akuzungulirani,+ 15 chifukwa Yehova Mulungu wanu amene ali pakati panu ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.+ Mukatsatira milungu ina, mkwiyo wa Yehova Mulungu wanu udzakuyakirani+ ndipo adzakufafanizani padziko lapansi.+
-