Yesaya 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Siliva amene munakutira mafano anu ogoba komanso golide amene munakutira mafano anu achitsulo,*+ mudzamuchititsa kuti akhale wonyansa. Mudzamutaya ngati mmene mkazi amene akusamba amatayira kansalu kake, ndipo mudzanena kuti: “Nyansi zimenezi!”+
22 Siliva amene munakutira mafano anu ogoba komanso golide amene munakutira mafano anu achitsulo,*+ mudzamuchititsa kuti akhale wonyansa. Mudzamutaya ngati mmene mkazi amene akusamba amatayira kansalu kake, ndipo mudzanena kuti: “Nyansi zimenezi!”+