Deuteronomo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene mukuchita. Iye akudziwa bwino kuti mukuyenda mʼchipululu chachikuluchi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi, ndipo simunasowe kanthu.”’+
7 Chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani pa chilichonse chimene mukuchita. Iye akudziwa bwino kuti mukuyenda mʼchipululu chachikuluchi. Yehova Mulungu wanu wakhala nanu zaka 40 zimenezi, ndipo simunasowe kanthu.”’+