Ekisodo 20:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ 4 Musadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba kapena chapadziko lapansi, kapenanso chamʼmadzi apadziko lapansi.+
3 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ 4 Musadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba kapena chapadziko lapansi, kapenanso chamʼmadzi apadziko lapansi.+