23 Kenako Yehova anauza Mose ndi Aroni mʼphiri la Hora, mʼmalire a dziko la Edomu kuti: 24 “Aroni aikidwa mʼmanda ngati mmene zinakhalira ndi makolo ake.+ Iye sadzalowa mʼdziko limene ndidzapatse Aisiraeli chifukwa awirinu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+