Deuteronomo 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse. Akanachita zimenezi zinthu zikanawayendera bwino, iwowo ndi ana awo mpaka kalekale!+
29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse. Akanachita zimenezi zinthu zikanawayendera bwino, iwowo ndi ana awo mpaka kalekale!+