Deuteronomo 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yehova anatilamula kuti tizitsatira malangizo onsewa komanso kuti tiziopa Yehova Mulungu wathu kuti zinthu zizitiyendera bwino nthawi zonse,+ komanso kuti tikhale ndi moyo+ ngati mmene zilili lero.
24 Ndiyeno Yehova anatilamula kuti tizitsatira malangizo onsewa komanso kuti tiziopa Yehova Mulungu wathu kuti zinthu zizitiyendera bwino nthawi zonse,+ komanso kuti tikhale ndi moyo+ ngati mmene zilili lero.