Deuteronomo 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukudziwa bwino mumtima mwanu kuti Yehova Mulungu wanu ankakulangizani, ngati mmene bambo amalangizira mwana wake.+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa Yehova* amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamuona kuti ndi mwana wake.”+
5 Inu mukudziwa bwino mumtima mwanu kuti Yehova Mulungu wanu ankakulangizani, ngati mmene bambo amalangizira mwana wake.+
6 Chifukwa Yehova* amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamuona kuti ndi mwana wake.”+