Deuteronomo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo muzipereka nsembe ya Pasika kwa Yehova Mulungu wanu.+ Muzipereka nkhosa ndi ngʼombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Deuteronomo 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mukatenge zina mwa zipatso zoyambirira pa zokolola* zonse zamʼmunda mwanu zimene mudzakolole mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani. Mukaziike mʼdengu nʼkupita nazo kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuika dzina lake.+
2 Ndipo muzipereka nsembe ya Pasika kwa Yehova Mulungu wanu.+ Muzipereka nkhosa ndi ngʼombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+
2 mukatenge zina mwa zipatso zoyambirira pa zokolola* zonse zamʼmunda mwanu zimene mudzakolole mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani. Mukaziike mʼdengu nʼkupita nazo kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuika dzina lake.+