Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo komanso zigamulo zolungama zofanana ndi Chilamulo chonsechi chimene ndikukupatsani lero?+ Deuteronomo 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la Chilamulo ichi, kuchokera mʼbuku limene* Alevi omwe ndi ansembe amasunga.+ Nehemiya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yesuwa, Bani, Serebiya,+ Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi,+ Hanani ndi Pelaya, omwe anali Alevi, ankafotokozera anthu Chilamulocho,+ anthuwo ataimirira.
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo komanso zigamulo zolungama zofanana ndi Chilamulo chonsechi chimene ndikukupatsani lero?+
18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la Chilamulo ichi, kuchokera mʼbuku limene* Alevi omwe ndi ansembe amasunga.+
7 Yesuwa, Bani, Serebiya,+ Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi,+ Hanani ndi Pelaya, omwe anali Alevi, ankafotokozera anthu Chilamulocho,+ anthuwo ataimirira.