Ekisodo 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzichita Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa.+ Mogwirizana ndi zimene ndinakulamulani, muzidya mikate yopanda zofufumitsa masiku 7 mʼmwezi wa Abibu* pa nthawi imene inaikidwa,+ chifukwa munatuluka mu Iguputo mʼmwezi wa Abibu.
18 Muzichita Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa.+ Mogwirizana ndi zimene ndinakulamulani, muzidya mikate yopanda zofufumitsa masiku 7 mʼmwezi wa Abibu* pa nthawi imene inaikidwa,+ chifukwa munatuluka mu Iguputo mʼmwezi wa Abibu.