2 Akorinto 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angakwanitse,+ osati zimene sangakwanitse.
12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angakwanitse,+ osati zimene sangakwanitse.