6 Mchimwene wanu, amene ndi mwana wamwamuna wa mayi anu, kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, mkazi wanu wokondedwa kapena mnzanu wapamtima, akayesa kukukopani mwachinsinsi pokuuzani kuti, ‘Tiyeni tikatumikire milungu ina,’+ milungu imene inuyo kapena makolo anu sankaidziwa,