Malaki 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu. Anthu ayenera kupita kwa iye kuti akamve Chilamulo*+ chifukwa iye ndi mthenga wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu. Anthu ayenera kupita kwa iye kuti akamve Chilamulo*+ chifukwa iye ndi mthenga wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.