Levitiko 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Malamulo angawa muziwasunga: Musamachititse kuti ziweto zanu zamitundu yosiyana zikwerane. Podzala mbewu mʼmunda mwanu musamasakanize mitundu iwiri yosiyana.+ Ndipo musamavale chovala cha ulusi wa mitundu iwiri yosakaniza.*+
19 Malamulo angawa muziwasunga: Musamachititse kuti ziweto zanu zamitundu yosiyana zikwerane. Podzala mbewu mʼmunda mwanu musamasakanize mitundu iwiri yosiyana.+ Ndipo musamavale chovala cha ulusi wa mitundu iwiri yosakaniza.*+