Ekisodo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona, ndamva kulira kwa Aisiraeli komanso ndaona nkhanza zimene Aiguputo akuwachitira powapondereza.+ Ekisodo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova akufuna kuthandiza Aisiraeli+ komanso kuti waona mavuto amene akukumana nawo,+ anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi. Machitidwe 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ine ndaona kuti anthu anga omwe ali ku Iguputo akuzunzidwa kwambiri. Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndabwera kudzawapulumutsa. Ndiye ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’
9 Taona, ndamva kulira kwa Aisiraeli komanso ndaona nkhanza zimene Aiguputo akuwachitira powapondereza.+
31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova akufuna kuthandiza Aisiraeli+ komanso kuti waona mavuto amene akukumana nawo,+ anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi.
34 Ine ndaona kuti anthu anga omwe ali ku Iguputo akuzunzidwa kwambiri. Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndabwera kudzawapulumutsa. Ndiye ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’