13 Asa ndi anthu amene anali naye anawathamangitsa mpaka kukafika ku Gerari+ ndipo anapitiriza kupha Aitiyopiyawo moti palibe amene anatsala ndi moyo, chifukwa Yehova ndi gulu lake anawagonjetseratu. Kenako anthuwo anatenga zinthu zambiri za Aitiyopiya.