-
Levitiko 26:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 ine ndidzakuchitani zotsatirazi: Ndidzakulangani pokupangitsani kukhala ndi mantha, kudwala chifuwa chachikulu ndi kutentha kwa thupi koopsa, zimene zidzachititsa maso anu khungu ndi kukufooketsani. Simudzapindula ndi mbewu zimene mwafesa, chifukwa adani anu adzadya zokolola zanuzo.+ 17 Ine ndidzakukanani, ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+
-