Amosi 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndinawononga mbewu zanu ndi mphepo yotentha komanso matenda a chuku.+ Munachulukitsa minda yanu ya mpesa ndi ya mbewu zina.Koma dzombe linawononga mitengo yanu ya mkuyu ndi ya maolivi,+Ndipo inu simunabwererebe kwa ine,’+ watero Yehova.
9 ‘Ndinawononga mbewu zanu ndi mphepo yotentha komanso matenda a chuku.+ Munachulukitsa minda yanu ya mpesa ndi ya mbewu zina.Koma dzombe linawononga mitengo yanu ya mkuyu ndi ya maolivi,+Ndipo inu simunabwererebe kwa ine,’+ watero Yehova.