16 Koma mʼmizinda ya anthu awa, imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, musalole kuti mutsale chamoyo chilichonse.+ 17 Mʼmalomwake, mudzawononge anthu onse. Mudzawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulamulani.