Deuteronomo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼchaka cha 40,+ mʼmwezi wa 11, pa tsiku loyamba la mweziwo, Mose anauza Aisiraeli* zonse zimene Yehova anamuuza kuti awauze. Deuteronomo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Awa ndi mawu a pangano limene Yehova analamula Mose kuti achite ndi Aisiraeli mʼdziko la Mowabu, kuwonjezera pa pangano limene anachita nawo ku Horebe.+
3 Mʼchaka cha 40,+ mʼmwezi wa 11, pa tsiku loyamba la mweziwo, Mose anauza Aisiraeli* zonse zimene Yehova anamuuza kuti awauze.
29 Awa ndi mawu a pangano limene Yehova analamula Mose kuti achite ndi Aisiraeli mʼdziko la Mowabu, kuwonjezera pa pangano limene anachita nawo ku Horebe.+