-
Deuteronomo 7:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Musabweretse mʼnyumba mwanu zinthu zonyansa kuti nanunso musakhale oyenera kuwonongedwa mofanana ndi zinthuzo. Muzinyansidwa nazo kwambiri komanso kuipidwa nazo chifukwa zinthu zimenezi ndi zoyenera kuwonongedwa.”
-