Yoswa 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo mukakangolanda mzindawo, mukauyatse moto.+ Mukachite zimenezi mogwirizana ndi mawu a Yehova. Ndakulamulani kuti mukachite zimenezi.”
8 Ndipo mukakangolanda mzindawo, mukauyatse moto.+ Mukachite zimenezi mogwirizana ndi mawu a Yehova. Ndakulamulani kuti mukachite zimenezi.”