Yoswa 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Mzinda wa Yeriko ndaupereka mʼmanja mwako, pamodzi ndi mfumu yake ndi asilikali ake amphamvu.+ Yoswa 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi anthu okalamba omwe. Anaphanso ngʼombe, nkhosa ndi abulu.+
2 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Mzinda wa Yeriko ndaupereka mʼmanja mwako, pamodzi ndi mfumu yake ndi asilikali ake amphamvu.+
21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi anthu okalamba omwe. Anaphanso ngʼombe, nkhosa ndi abulu.+