Deuteronomo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nyamukani ndipo muwoloke chigwa cha Arinoni.*+ Taonani, ndapereka mʼmanja mwanu Sihoni+ yemwe ndi munthu wa Chiamori, mfumu ya Hesiboni. Choncho yambani kulanda dziko lake ndipo muchite naye nkhondo.
24 Nyamukani ndipo muwoloke chigwa cha Arinoni.*+ Taonani, ndapereka mʼmanja mwanu Sihoni+ yemwe ndi munthu wa Chiamori, mfumu ya Hesiboni. Choncho yambani kulanda dziko lake ndipo muchite naye nkhondo.