35 Anthu onse okhala padziko lapansi ndi opanda pake poyerekezera ndi Mulungu. Iye amachita zinthu mogwirizana ndi zofuna zake pakati pa magulu akumwamba ndi anthu okhala padziko lapansi. Palibe aliyense amene angamulepheretse kuchita zimene akufuna+ kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+