Deuteronomo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yairi+ mwana wamwamuna wa Manase anatenga dera lonse la Arigobi+ mpaka kumalire a Agesuri ndi a Amaakati.+ Midzi ya ku Basana imeneyo anaipatsa dzina lofanana ndi lake lakuti, Havoti-yairi*+ ndipo imadziwika ndi dzina limeneli mpaka pano.
14 Yairi+ mwana wamwamuna wa Manase anatenga dera lonse la Arigobi+ mpaka kumalire a Agesuri ndi a Amaakati.+ Midzi ya ku Basana imeneyo anaipatsa dzina lofanana ndi lake lakuti, Havoti-yairi*+ ndipo imadziwika ndi dzina limeneli mpaka pano.