Numeri 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati Yehova akusangalala nafe, adzatilowetsadi mʼdzikolo nʼkulipereka kwa ife, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Deuteronomo 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova Mulungu wanu adzathamangitsira mitundu imeneyi kutali ndi inu, kuichotsa pamaso panu pangʼonopangʼono.+ Sadzakulolani kuti muiwononge mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingachuluke nʼkukuwonongani. Deuteronomo 33:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiwe wosangalala iwe Isiraeli!+ Ndani angafanane ndi iwe,+Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+Chishango chako chokuteteza,+Komanso lupanga lako lamphamvu? Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+Ndipo iwe udzaponda pamisana yawo.”*
8 Ngati Yehova akusangalala nafe, adzatilowetsadi mʼdzikolo nʼkulipereka kwa ife, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+
22 Yehova Mulungu wanu adzathamangitsira mitundu imeneyi kutali ndi inu, kuichotsa pamaso panu pangʼonopangʼono.+ Sadzakulolani kuti muiwononge mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingachuluke nʼkukuwonongani.
29 Ndiwe wosangalala iwe Isiraeli!+ Ndani angafanane ndi iwe,+Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+Chishango chako chokuteteza,+Komanso lupanga lako lamphamvu? Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+Ndipo iwe udzaponda pamisana yawo.”*