Deuteronomo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nʼchifukwa chake fuko la Levi silinapatsidwe gawo kapena cholowa ngati abale awo. Cholowa chawo ndi Yehova, mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anawauza.+ Deuteronomo 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Alevi omwe ndi ansembe, komanso fuko lonse la Levi, sadzapatsidwa gawo kapena cholowa pakati pa Aisiraeli. Iwo azidzadya nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, zomwe ndi cholowa chake.+
9 Nʼchifukwa chake fuko la Levi silinapatsidwe gawo kapena cholowa ngati abale awo. Cholowa chawo ndi Yehova, mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anawauza.+
18 “Alevi omwe ndi ansembe, komanso fuko lonse la Levi, sadzapatsidwa gawo kapena cholowa pakati pa Aisiraeli. Iwo azidzadya nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, zomwe ndi cholowa chake.+